MVUNGUTI
BOOKS Mvunguti Books, sister to the Kachere Series, publishes books in the many languages of Malawi, and since English has become one of them, it is not excluded either. While most of the teaching of theology in Malawi is done in English, most of the preaching, singing and praying is done in the many different languages of Malawi, so the Mvunguti Books intend to develop vernacular theology in Malawi and also to publish cultural texts. |
||
SANGAYA:
Mtsogoleri wa Sinodi ya Blantyre Mpingo wa CCAP |
||
PA CHIYAMBI ANAWALENGA CHIMODZIMODZI |
||
MOYO
NDI UTUMIKI WA MBUSA NDI MAI MOUCHA WA PROVIDENCE INDUSTRIAL MISSION Patrick Makondesa Text in Chichewa Mbiri ya Mpingo wa Providence Industrial Mission (PIM) ndi yodziwika kwambiri kupyolera mwamstogoleri wake woyamba Mbusa John Chilembwe amene anaphedwa m'chaka cha 1915. Dr. Daniel Malekebu ndi mkazi wake Flora analowa m'malo mwake m'chaka cha 1926. Bukuli likulongosola moyo ndi utumiki wa Mbusa Muocha ndi mkazi wake amene anatsatira Dr. Malekebu ndi mkazi wake (1971-1987). ISBN 9908-16-31-X, Mvunguti Book No. 3, 2000 |
||
NTHANTHI
ZA CHITONGA ZA KUSAMBIZGIYA NDI KUTAULIYA David Mphande Text in Chitonga Proverbs are a never-ending treasure of wisdom for any people. In this book, written entirely in Chitonga, David Mphande presents 200 proverbs and explores how each of them can be used in preaching and teaching. ISBN 99908-16-36-0, Mvunguti Book No. 5, 2000 |
||
MTUMWI
PAULO NDI UDINDO WA AMAYI MUMPINGO Janet Y. Kholowa ndi Klaus Fiedler Text in Chichewa Kuno ku Malawi nkhani yakulalikira kwa amayi mtchalitchi ili mkamwamkamwa. Ena amakana, ena amavomereza, onse amatsimikiza kuti amatsatila Baibulo. Bukuli lafufuza mozama zimene Mtumwi Paulo anachita ndi kunena zokhudza udindo wa amayi mu tchalitchi. ISBN 9908-16-31-X, Mvunguti Book No. 6, 2001 |
||
CHIKONZEDWE
CHA MPINGO: Zosintha zazikulu za uzimu 1500-1650 Steven Paas Text in Chichewa Bukuli limafotokozera mbiri ya Nyengo ya Chikonzedwe cha Mpingo ku maiko a ku Ulaya m'zaka za 1500-1650. Nyengoyi inali nthawi ya kusintha kwakukulu imene inatsegula chitseko cha tsogolo latsopano, ndiponso nthawiyi inagwedeza anthu. Anthu anafufuza mafunso pa zovuta zambiri. Panthawiyi Mulungu anatumiza nthumwi za Mpingo wake, kuti zitsogolere anthu kuwerenga ndi kutsatira Baibulo. Ntchito ya Chikonzedwechi inatsitsimutsa Mpingo. Zaka zambiri zitatha, mipingo ya ku Ulaya, kudzera m'ntchito ya Mishoni, inabweretsa Baibulo ku Africa, komwe kunakhazikitsidwa Mipingo yambiri. Anthu amene akufuna kumva bwino Mbiri ya Mpingo ya ku Africa ayenera kudziwa Mbiri ya Chikonzedwechi. Ichi ndi cholinga chake cha bukuli. ISBN 99908-16-47-6, Mvunguti Book No. 7, 2002 |
||
THE GOD OF LOVE
AND COMPASSION: A CHRISTIAN MEDITATION ON AIDS |
||
|
||
Journals
and African Languages books are only |
||
For
book orders outside of Africa please contact |
||
For orders within Africa contact |
||
HOME
| NEW | BOOKS
| MONOGRAPHS | TEXTS |
STUDIES | THESES
| AFRICAN LANGUAGES | |